![](https://mwnation.com/wp-content/uploads/2023/10/arrested.jpg)
Woganiziridwa kuzembetsa anthu wagwidwa
Mwambi woti khoswe wa pa tsindwi adaulula wa pa dzala wapherezera ku Mulanje komwe mlandu wa pa msewu wavumbulutsa mulandu wozembetsa anthu. Malingana ndi mneneri was apolisi m’boma la Mulanje a Innocent Moses, kugwidwa kwa dilaiva yemwe minibasi yake …