
Okonda a Chakwera yang’anani kumbali: a Malawi ochuluka akufuna APM abwelere
N’kuthekadi kuti chitsime chimadziwika ndi chakuya pamene chaphwera, chifukwa a Malawi ochuluka akuti bola kwa Farao komwe kuja. Ulendo wa ku Kenani ati aulephera ndipo iwo ndi okonzeka kubwelera. Mtsogoleri wa kale a Peter Mutharika akuoneka ali ndi …